1 Samueli 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Amuna amenewa anatichitira zabwino kwambiri, sanativutitse, moti masiku onse amene tinali kuyenda nawo kutchire sitinataye kanthu ngakhale kamodzi.+ Luka 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso, asilikali anali kumufunsa kuti: “Nanga ife tichite chiyani?” Iye anali kuwauza kuti: “Musamavutitse anthu kapena kunamizira+ aliyense, koma muzikhutira ndi zimene mumalandira.”+
15 Amuna amenewa anatichitira zabwino kwambiri, sanativutitse, moti masiku onse amene tinali kuyenda nawo kutchire sitinataye kanthu ngakhale kamodzi.+
14 Komanso, asilikali anali kumufunsa kuti: “Nanga ife tichite chiyani?” Iye anali kuwauza kuti: “Musamavutitse anthu kapena kunamizira+ aliyense, koma muzikhutira ndi zimene mumalandira.”+