1 Samueli 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo Nabala anayankha atumiki a Davide kuti: “Kodi Davide ndani,+ ndipo mwana wa Jese ndani? Masiku ano atumiki amene akuthawa ambuye awo achuluka kwabasi.+ Salimo 35:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Adani anga amandibwezera zoipa m’malo mwa zabwino,+Ndipo ndimakhala wachisoni ngati wofedwa.+ Salimo 38:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iwo anali kundibwezera choipa m’malo mwa chabwino,+Ndikamayesetsa kuchita chabwino anali kunditsutsa.+ Salimo 109:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikawachitira zabwino amandibwezera zoipa,+Ndikawasonyeza chikondi amandibwezera chidani.+ Miyambo 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Aliyense wobwezera zoipa pa zabwino,+ zoipa sizidzachoka panyumba pake.+
10 Pamenepo Nabala anayankha atumiki a Davide kuti: “Kodi Davide ndani,+ ndipo mwana wa Jese ndani? Masiku ano atumiki amene akuthawa ambuye awo achuluka kwabasi.+
20 Iwo anali kundibwezera choipa m’malo mwa chabwino,+Ndikamayesetsa kuchita chabwino anali kunditsutsa.+