1 Samueli 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye anapitiriza kuuza Davide kuti: “Ndiwe wolungama kwambiri kuposa ine,+ pakuti iwe wandichitira zabwino,+ koma ine ndakuchitira zoipa. Salimo 38:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iwo anali kundibwezera choipa m’malo mwa chabwino,+Ndikamayesetsa kuchita chabwino anali kunditsutsa.+ Yeremiya 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kodi zabwino amazibwezera ndi zoipa?+ Kumbukirani nthawi zonse zija pamene ndinaima pamaso panu kuwalankhulira zabwino kuti muwachotsere mkwiyo wanu.+ Koma iwo tsopano andikumbira mbuna.+
17 Iye anapitiriza kuuza Davide kuti: “Ndiwe wolungama kwambiri kuposa ine,+ pakuti iwe wandichitira zabwino,+ koma ine ndakuchitira zoipa.
20 Iwo anali kundibwezera choipa m’malo mwa chabwino,+Ndikamayesetsa kuchita chabwino anali kunditsutsa.+
20 Kodi zabwino amazibwezera ndi zoipa?+ Kumbukirani nthawi zonse zija pamene ndinaima pamaso panu kuwalankhulira zabwino kuti muwachotsere mkwiyo wanu.+ Koma iwo tsopano andikumbira mbuna.+