1 Samueli 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Poyankha Sauli anati: “Ndachimwa.+ Bwerera mwana wanga Davide, pakuti sindidzakuvulaza chifukwa moyo wanga wakhala wamtengo wapatali+ kwa iwe lero. Taona, ndachita zinthu mopusa ndipo ndalakwitsa kwambiri.”
21 Poyankha Sauli anati: “Ndachimwa.+ Bwerera mwana wanga Davide, pakuti sindidzakuvulaza chifukwa moyo wanga wakhala wamtengo wapatali+ kwa iwe lero. Taona, ndachita zinthu mopusa ndipo ndalakwitsa kwambiri.”