Ekisodo 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako Farao anatumiza atumiki ake kukaitana Mose ndi Aroni ndi kuwauza kuti: “Tsopano ndachimwa.+ Yehova ndi wolungama,+ koma ine ndi anthu anga ndife olakwa. 1 Samueli 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pamenepo Sauli anayankha Samueli kuti: “Ndachimwa,+ ndaphwanya lamulo la Yehova komanso sindinamvere mawu anu, chifukwa ndinaopa anthu+ ndipo ndamvera mawu awo. 1 Samueli 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye anapitiriza kuuza Davide kuti: “Ndiwe wolungama kwambiri kuposa ine,+ pakuti iwe wandichitira zabwino,+ koma ine ndakuchitira zoipa. Mateyu 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye anati: “Ndachimwa popereka munthu wolungama.”*+ Koma iwo anamuyankha kuti: “Ife sizikutikhudza zimenezo. Udziwa wekha chochita!”+
27 Kenako Farao anatumiza atumiki ake kukaitana Mose ndi Aroni ndi kuwauza kuti: “Tsopano ndachimwa.+ Yehova ndi wolungama,+ koma ine ndi anthu anga ndife olakwa.
24 Pamenepo Sauli anayankha Samueli kuti: “Ndachimwa,+ ndaphwanya lamulo la Yehova komanso sindinamvere mawu anu, chifukwa ndinaopa anthu+ ndipo ndamvera mawu awo.
17 Iye anapitiriza kuuza Davide kuti: “Ndiwe wolungama kwambiri kuposa ine,+ pakuti iwe wandichitira zabwino,+ koma ine ndakuchitira zoipa.
4 Iye anati: “Ndachimwa popereka munthu wolungama.”*+ Koma iwo anamuyankha kuti: “Ife sizikutikhudza zimenezo. Udziwa wekha chochita!”+