Salimo 129:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova ndi wolungama.+Iye waduladula zingwe za oipa.+ Salimo 145:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova ndi wolungama m’njira zake zonse,+Ndipo ndi wokhulupirika m’ntchito zake zonse.+ Danieli 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Inu Yehova, munakhala tcheru kuti mutigwetsere tsoka ndipo pamapeto pake munatigwetseradi tsokalo,+ pakuti inu Yehova Mulungu wathu ndinu wolungama pa ntchito zanu zonse zimene mwachita, koma ife sitinamvere mawu anu.+ Aroma 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma chifukwa chakuti ndiwe wosafuna kusintha khalidwe+ ndiponso wa mtima wosalapa,+ ukudzisungira mkwiyo wa Mulungu.+ Mulungu adzasonyeza mkwiyo+ umenewu pa tsiku loulula+ chiweruzo chake cholungama.+
14 “Inu Yehova, munakhala tcheru kuti mutigwetsere tsoka ndipo pamapeto pake munatigwetseradi tsokalo,+ pakuti inu Yehova Mulungu wathu ndinu wolungama pa ntchito zanu zonse zimene mwachita, koma ife sitinamvere mawu anu.+
5 Koma chifukwa chakuti ndiwe wosafuna kusintha khalidwe+ ndiponso wa mtima wosalapa,+ ukudzisungira mkwiyo wa Mulungu.+ Mulungu adzasonyeza mkwiyo+ umenewu pa tsiku loulula+ chiweruzo chake cholungama.+