Salimo 124:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Moyo wathu uli ngati mbalame imene yathawa+Pamsampha wa munthu wogwiritsa ntchito nyambo.+Msamphawo wathyoka,+Ndipo ife tapulumuka.+ Salimo 140:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu odzikweza anditchera msampha.+Iwo aika zingwe ponseponse ngati ukonde m’mphepete mwa njira,+Ndipo anditchera makhwekhwe.+ [Seʹlah.]
7 Moyo wathu uli ngati mbalame imene yathawa+Pamsampha wa munthu wogwiritsa ntchito nyambo.+Msamphawo wathyoka,+Ndipo ife tapulumuka.+
5 Anthu odzikweza anditchera msampha.+Iwo aika zingwe ponseponse ngati ukonde m’mphepete mwa njira,+Ndipo anditchera makhwekhwe.+ [Seʹlah.]