Salimo 119:110 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 110 Oipa anditchera msampha,+Koma ine sindinasochere ndi kuchoka pa malamulo anu.+ Salimo 141:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nditetezeni kuti ndisagwidwe pamsampha umene anditchera,+Kuti ndisakodwe ndi makhwekhwe a anthu ochita zopweteka anzawo.+
9 Nditetezeni kuti ndisagwidwe pamsampha umene anditchera,+Kuti ndisakodwe ndi makhwekhwe a anthu ochita zopweteka anzawo.+