Salimo 140:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu odzikweza anditchera msampha.+Iwo aika zingwe ponseponse ngati ukonde m’mphepete mwa njira,+Ndipo anditchera makhwekhwe.+ [Seʹlah.] Salimo 141:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nditetezeni kuti ndisagwidwe pamsampha umene anditchera,+Kuti ndisakodwe ndi makhwekhwe a anthu ochita zopweteka anzawo.+ Salimo 142:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinachita zimenezi pamene mtima wanga+ unalefuka.Pamenepo, munadziwa njira yanga.+Adani anga anditchera msampha+M’njira imene ndikuyenda.+
5 Anthu odzikweza anditchera msampha.+Iwo aika zingwe ponseponse ngati ukonde m’mphepete mwa njira,+Ndipo anditchera makhwekhwe.+ [Seʹlah.]
9 Nditetezeni kuti ndisagwidwe pamsampha umene anditchera,+Kuti ndisakodwe ndi makhwekhwe a anthu ochita zopweteka anzawo.+
3 Ndinachita zimenezi pamene mtima wanga+ unalefuka.Pamenepo, munadziwa njira yanga.+Adani anga anditchera msampha+M’njira imene ndikuyenda.+