Salimo 119:110 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 110 Oipa anditchera msampha,+Koma ine sindinasochere ndi kuchoka pa malamulo anu.+ Salimo 124:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Moyo wathu uli ngati mbalame imene yathawa+Pamsampha wa munthu wogwiritsa ntchito nyambo.+Msamphawo wathyoka,+Ndipo ife tapulumuka.+
7 Moyo wathu uli ngati mbalame imene yathawa+Pamsampha wa munthu wogwiritsa ntchito nyambo.+Msamphawo wathyoka,+Ndipo ife tapulumuka.+