Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 23:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Kenako Sauli anakhala mbali imodzi ya phiri ndipo Davide ndi amuna amene anali kuyenda naye anali mbali inanso ya phirilo. Zitatero Davide ananyamuka mofulumira kuti athawe+ Sauli. Pa nthawiyi n’kuti Sauli ndi asilikali ake atatsala pang’ono kupeza ndi kugwira Davide ndi amuna amene anali kuyenda naye.+

  • 2 Samueli 17:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Nthawi yomweyo Davide ananyamuka pamodzi ndi anthu onse amene anali naye, ndipo anawoloka Yorodano mpaka m’mawa.+ Onse anawoloka Yorodano popanda wotsala.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena