Salimo 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amadikirira anthu pamalo obisika ngati mkango pamalo ake obisalapo.+Amawadikirira+ kuti atenge mokakamiza munthu wosautsika.Amakulunga wosautsika mu ukonde wake ndi kumutenga mokakamiza.+ Salimo 35:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo andikumbira mbuna popanda chifukwa ndi kuikapo ukonde,+Akumba mbunazo kuti ndigweremo ngakhale kuti sindinalakwe.+ Salimo 57:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwo anditchera ukonde panjira yanga.+Moyo wanga wagwidwa ndi chisoni.+Andikumbira mbuna.Koma iwo agweramo.+ [Seʹlah.]
9 Amadikirira anthu pamalo obisika ngati mkango pamalo ake obisalapo.+Amawadikirira+ kuti atenge mokakamiza munthu wosautsika.Amakulunga wosautsika mu ukonde wake ndi kumutenga mokakamiza.+
7 Iwo andikumbira mbuna popanda chifukwa ndi kuikapo ukonde,+Akumba mbunazo kuti ndigweremo ngakhale kuti sindinalakwe.+
6 Iwo anditchera ukonde panjira yanga.+Moyo wanga wagwidwa ndi chisoni.+Andikumbira mbuna.Koma iwo agweramo.+ [Seʹlah.]