Deuteronomo 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Muyenera kudziwa kuti Yehova Mulungu wanu akukupatsani dziko labwinoli osati chifukwa cha kulungama kwanu, pakuti ndinu anthu ouma khosi.+ Ezekieli 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma a nyumba ya Isiraeli sakafuna kukumvera, chifukwa iwo safuna kundimvera.+ Pakuti anthu onse a nyumba ya Isiraeli ndi amakani ndi osamva.+
6 Muyenera kudziwa kuti Yehova Mulungu wanu akukupatsani dziko labwinoli osati chifukwa cha kulungama kwanu, pakuti ndinu anthu ouma khosi.+
7 Koma a nyumba ya Isiraeli sakafuna kukumvera, chifukwa iwo safuna kundimvera.+ Pakuti anthu onse a nyumba ya Isiraeli ndi amakani ndi osamva.+