1 Samueli 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Poyankha, Yehova anauza Samueli+ kuti: “Mvera zonse zimene anthuwo akunena kwa iwe,+ pakuti sanakane iweyo koma akana ine kuti ndisakhale mfumu yawo.+ Yeremiya 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Koma simunandimvere,’ watero Yehova, ‘ndipo munachita zimenezo n’cholinga chondikhumudwitsa ndi mafano anu. Zimenezi zakubweretserani tsoka.’+ Luka 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Amene akukumverani,+ akumveranso ine. Ndipo amene akunyalanyaza+ inu akunyalanyazanso ine. Ndipotu amene akunyalanyaza ine akunyalanyazanso amene anandituma.”
7 Poyankha, Yehova anauza Samueli+ kuti: “Mvera zonse zimene anthuwo akunena kwa iwe,+ pakuti sanakane iweyo koma akana ine kuti ndisakhale mfumu yawo.+
7 “‘Koma simunandimvere,’ watero Yehova, ‘ndipo munachita zimenezo n’cholinga chondikhumudwitsa ndi mafano anu. Zimenezi zakubweretserani tsoka.’+
16 “Amene akukumverani,+ akumveranso ine. Ndipo amene akunyalanyaza+ inu akunyalanyazanso ine. Ndipotu amene akunyalanyaza ine akunyalanyazanso amene anandituma.”