Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 8:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Koma Gidiyoni anawayankha kuti: “Ineyo sindikhala wokulamulirani, ngakhalenso mwana wanga sakhala wokulamulirani.+ Yehova ndiye azikulamulirani.”+

  • 1 Samueli 10:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Koma inu, lero mwakana Mulungu wanu+ amene anakupulumutsani m’masautso anu onse ndi m’zowawa zanu, kufika ponena kuti: “Ife tikufuna kuti utiikire mfumu yoti izitilamulira.” Tsopano imani pamaso pa Yehova malinga ndi mafuko anu+ ndi mabanja anu.’”*

  • 1 Samueli 12:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mutaona kuti mfumu ya ana a Amoni, Nahasi,+ yabwera kudzamenyana nanu, munayamba kundiuza kuti, ‘Ife tikufuna kuti mfumu izitilamulira!’+ ngakhale kuti Yehova Mulungu wanu ndiye Mfumu yanu.+

  • Salimo 74:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Koma Mulungu ndi Mfumu yanga kuyambira kalekale,+

      Iye ndiye wondipatsa chipulumutso chachikulu padziko lapansi.+

  • Yesaya 33:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pakuti Yehova ndiye Woweruza wathu.+ Yehova ndiye Wotipatsa Malamulo.+ Yehova ndiye Mfumu yathu.+ Iye adzatipulumutsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena