2 Samueli 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Munthu wokhulupirika, mudzamuchitira mokhulupirika.+Munthu wamphamvu wopanda cholakwa, mudzamuchitira mwachilungamo.+ Miyambo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 mwa kuyang’anitsitsa njira zachiweruzo,+ ndipo adzateteza njira ya anthu ake okhulupirika.+
26 Munthu wokhulupirika, mudzamuchitira mokhulupirika.+Munthu wamphamvu wopanda cholakwa, mudzamuchitira mwachilungamo.+ Miyambo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 mwa kuyang’anitsitsa njira zachiweruzo,+ ndipo adzateteza njira ya anthu ake okhulupirika.+