Salimo 44:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu Mulungu, ndinu Mfumu yanga.+Lamulani kuti Yakobo alandire chipulumutso chachikulu.+ Salimo 74:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Mulungu ndi Mfumu yanga kuyambira kalekale,+Iye ndiye wondipatsa chipulumutso chachikulu padziko lapansi.+ Salimo 97:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 97 Yehova wakhala mfumu!+ Dziko lapansi likondwere,+Ndipo zilumba zambiri zisangalale.+ Chivumbulutso 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ndi mawu akuti: “Tikukuyamikani+ inu Yehova, Mulungu Wamphamvuyonse,+ Inu amene mulipo+ ndi amene munalipo, chifukwa mwatenga mphamvu yanu yaikulu+ ndi kuyamba kulamulira monga mfumu.+ Chivumbulutso 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ndinamva mawu ngati a khamu lalikulu, omveka ngati mkokomo wa madzi ambiri ndi mabingu amphamvu. Mawuwo anati: “Tamandani Ya,+ anthu inu, chifukwa Yehova* Mulungu wathu, Wamphamvuyonse,+ wayamba kulamulira monga mfumu.+
12 Koma Mulungu ndi Mfumu yanga kuyambira kalekale,+Iye ndiye wondipatsa chipulumutso chachikulu padziko lapansi.+
17 ndi mawu akuti: “Tikukuyamikani+ inu Yehova, Mulungu Wamphamvuyonse,+ Inu amene mulipo+ ndi amene munalipo, chifukwa mwatenga mphamvu yanu yaikulu+ ndi kuyamba kulamulira monga mfumu.+
6 Kenako ndinamva mawu ngati a khamu lalikulu, omveka ngati mkokomo wa madzi ambiri ndi mabingu amphamvu. Mawuwo anati: “Tamandani Ya,+ anthu inu, chifukwa Yehova* Mulungu wathu, Wamphamvuyonse,+ wayamba kulamulira monga mfumu.+