Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mulungu anamuyankha Mose kuti: “NDIDZAKHALA AMENE NDIDZAFUNE KUKHALA.”+ Ndiyeno anawonjezera kuti: “Ana a Isiraeli ukawauze kuti, ‘NDIDZAKHALA AMENE NDIDZAFUNE KUKHALA ndiye wandituma kwa inu.’”+

  • Chivumbulutso 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ine Yohane, ndikulembera mipingo 7+ ya m’chigawo cha Asia.

      Kukoma mtima kwakukulu, ndi mtendere zikhale nanu kuchokera kwa “Iye amene alipo, amene analipo, ndi amene akubwera,”+ ndiponso kuchokera kwa mizimu 7+ yokhala pamaso pa mpando wake wachifumu.

  • Chivumbulutso 16:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiye ndinamva mngelo wokhala ndi ulamuliro pa madzi akunena kuti: “Inu Amene mulipo ndi amene munalipo,+ inu Wokhulupirika,+ ndinu wolungama chifukwa mwapereka zigamulo zimenezi,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena