Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 11:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Ine ndine Yehova amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo kuti ndikusonyezeni kuti ndine Mulungu.+ Muzikhala oyera,+ chifukwa ine ndine woyera.+

  • Yobu 23:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Iye ali ndi maganizo amodzi, ndani angam’tsutse?+

      Zimene moyo wake umalakalaka amazichita.+

  • Yesaya 14:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Pakuti Yehova wa makamu wagamula,+ ndani angazilepheretse?+ Dzanja lake n’limene latambasuka, ndani angalibweze?+

  • Danieli 4:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Iye amaona anthu onse okhala padziko lapansi ngati opanda pake+ ndipo amachita zinthu mogwirizana ndi chifuniro chake pakati pa makamu akumwamba ndi pakati pa anthu okhala padziko lapansi.+ Palibe aliyense amene angaletse dzanja+ lake kapena kumufunsa kuti, ‘Mukuchita chiyani?’+

  • Yohane 12:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Atate lemekezani dzina lanu.” Pamenepo mawu+ anamveka kuchokera kumwamba kuti: “Ndalilemekeza ndipo ndidzalilemekezanso.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena