Yobu 34:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iye amaphwanya amphamvu+ popanda kuwafufuza,Ndipo amachititsa ena kuima m’malo mwawo.+ Yesaya 43:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Komanso, nthawi zonse ine sindisintha.+ Palibenso wina amene angathe kupulumutsa anthu m’dzanja langa.+ Ndikayamba kuchitapo kanthu,+ ndani amene angalimbane ndi dzanja langa?”+ 1 Akorinto 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kapena “kodi tikufuna kuputa nsanje+ ya Yehova”? Kodi mphamvu zathu zingafanane ndi zake?+
13 “Komanso, nthawi zonse ine sindisintha.+ Palibenso wina amene angathe kupulumutsa anthu m’dzanja langa.+ Ndikayamba kuchitapo kanthu,+ ndani amene angalimbane ndi dzanja langa?”+