Deuteronomo 32:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Onani tsopano kuti ndine Mulungu,+Ndipo palibe milungu ina pamodzi ndi ine.+Ndimapha ndiponso ndimapereka moyo.+Ndavulaza koopsa,+ ndipo ine ndidzachiritsa,+Palibe aliyense wonditsomphola m’dzanja langa.+ Salimo 50:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zindikirani zimenezi, anthu oiwala Mulungu inu,+Kuti ndisakukhadzulekhadzuleni popanda aliyense wokupulumutsani.+ Hoseya 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano ndidzamuvula kuti amuna omukonda kwambiriwo aone maliseche ake,+ ndipo palibe mwamuna amene adzamukwatula m’dzanja langa.+
39 Onani tsopano kuti ndine Mulungu,+Ndipo palibe milungu ina pamodzi ndi ine.+Ndimapha ndiponso ndimapereka moyo.+Ndavulaza koopsa,+ ndipo ine ndidzachiritsa,+Palibe aliyense wonditsomphola m’dzanja langa.+
22 Zindikirani zimenezi, anthu oiwala Mulungu inu,+Kuti ndisakukhadzulekhadzuleni popanda aliyense wokupulumutsani.+
10 Tsopano ndidzamuvula kuti amuna omukonda kwambiriwo aone maliseche ake,+ ndipo palibe mwamuna amene adzamukwatula m’dzanja langa.+