Yeremiya 13:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndidzakuvula siketi yako ndi kukuphimba nayo kumaso, moti udzachita manyazi.+ Ezekieli 16:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 ine ndisonkhanitsa pamodzi zibwenzi zako zonse zimene unali kuzisangalatsa. Ndisonkhanitsanso anthu onse ochokera kumalo onse okuzungulira amene unali kuwakonda limodzi ndi onse amene unali kudana nawo kuti akuukire. Ndidzakuvula pamaso pawo ndipo iwo adzaona maliseche ako onse.+ Ezekieli 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iwo adzakulanga mwaukali ndi kukutengera zinthu zonse zimene unazipeza movutikira ndipo adzakusiya wosavala ndi wamaliseche.+ Umaliseche umene unauonetsa pochita dama, khalidwe lako lotayirira, ndi zochita zako zauhule zidzaonekera poyera.+
37 ine ndisonkhanitsa pamodzi zibwenzi zako zonse zimene unali kuzisangalatsa. Ndisonkhanitsanso anthu onse ochokera kumalo onse okuzungulira amene unali kuwakonda limodzi ndi onse amene unali kudana nawo kuti akuukire. Ndidzakuvula pamaso pawo ndipo iwo adzaona maliseche ako onse.+
29 Iwo adzakulanga mwaukali ndi kukutengera zinthu zonse zimene unazipeza movutikira ndipo adzakusiya wosavala ndi wamaliseche.+ Umaliseche umene unauonetsa pochita dama, khalidwe lako lotayirira, ndi zochita zako zauhule zidzaonekera poyera.+