Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliro 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Yerusalemu wachita tchimo+ lalikulu. N’chifukwa chake wakhala chinthu chonyansa.+

      Onse amene anali kumulemekeza ayamba kumuona ngati chinthu chachabechabe,+ chifukwa aona maliseche+ ake.

      Iyenso akuusa moyo+ ndipo watembenukira kwina chifukwa cha manyazi.

  • Ezekieli 16:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 ine ndisonkhanitsa pamodzi zibwenzi zako zonse zimene unali kuzisangalatsa. Ndisonkhanitsanso anthu onse ochokera kumalo onse okuzungulira amene unali kuwakonda limodzi ndi onse amene unali kudana nawo kuti akuukire. Ndidzakuvula pamaso pawo ndipo iwo adzaona maliseche ako onse.+

  • Ezekieli 23:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Iwo adzakulanga mwaukali ndi kukutengera zinthu zonse zimene unazipeza movutikira ndipo adzakusiya wosavala ndi wamaliseche.+ Umaliseche umene unauonetsa pochita dama, khalidwe lako lotayirira, ndi zochita zako zauhule zidzaonekera poyera.+

  • Hoseya 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsopano ndidzamuvula kuti amuna omukonda kwambiriwo aone maliseche ake,+ ndipo palibe mwamuna amene adzamukwatula m’dzanja langa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena