Deuteronomo 28:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Iwo adzadya chipatso cha ziweto zako ndi zipatso za nthaka yako kufikira utafafanizidwa,+ ndipo sadzakusiyirako mbewu, vinyo watsopano kapena mafuta, mwana wa ng’ombe yako kapena mwana wa nkhosa yako kufikira atakuwonongeratu.+ Ezekieli 16:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndidzakupereka m’manja mwa anthu okuukira ndipo iwo adzafafaniza mulu wako wadothi+ ndi malo ako okwera.+ Iwo adzakuvula zovala+ ndipo adzatenga zinthu zako zokongola+ n’kukusiya wosavala ndi wamaliseche.
51 Iwo adzadya chipatso cha ziweto zako ndi zipatso za nthaka yako kufikira utafafanizidwa,+ ndipo sadzakusiyirako mbewu, vinyo watsopano kapena mafuta, mwana wa ng’ombe yako kapena mwana wa nkhosa yako kufikira atakuwonongeratu.+
39 Ndidzakupereka m’manja mwa anthu okuukira ndipo iwo adzafafaniza mulu wako wadothi+ ndi malo ako okwera.+ Iwo adzakuvula zovala+ ndipo adzatenga zinthu zako zokongola+ n’kukusiya wosavala ndi wamaliseche.