Levitiko 26:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndikadzathyola ndodo zanu zopachikapo mkate wozungulira woboola pakati,+ akazi 10 adzaphika mkate mu uvuni umodzi, ndipo adzakugawirani mochita kukuyezerani pamuyezo.+ Chotero mudzadya koma simudzakhuta.+ Yeremiya 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndidzapereka chuma chanu anthu inu ndi zinthu zanu zamtengo wapatali kwa wofunkha+ popanda malipiro. Ndidzatero chifukwa cha machimo anu onse amene munachita m’dziko lanu lonse.+
26 Ndikadzathyola ndodo zanu zopachikapo mkate wozungulira woboola pakati,+ akazi 10 adzaphika mkate mu uvuni umodzi, ndipo adzakugawirani mochita kukuyezerani pamuyezo.+ Chotero mudzadya koma simudzakhuta.+
13 Ndidzapereka chuma chanu anthu inu ndi zinthu zanu zamtengo wapatali kwa wofunkha+ popanda malipiro. Ndidzatero chifukwa cha machimo anu onse amene munachita m’dziko lanu lonse.+