Yesaya 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu adzacheka kumbali yake yakumanja, koma adzakhala ndi njala. Adzadya kumanzere kwake, koma sadzakhuta.+ Aliyense adzadya mnofu wa dzanja lake.+ Mika 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inuyo mudzadya koma simudzakhuta ndipo mudzamvabe njala.+ Mudzanyamula zinthu kuti mukazisunge pabwino koma simudzatha kuziteteza. Zinthu zilizonse zimene mudzazitenge, ine ndidzazipereka kwa adani anu kuti aziwononge.+ Hagai 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwafesa mbewu zambiri koma zokolola zanu n’zochepa.+ Mukudya koma simukukhuta.+ Mukumwa koma simukukhutira.* Mukuvala zovala koma simukumva kutentha. Amene akugwira ganyu akulandirira ndalama zake m’matumba obowoka.’”+
20 Munthu adzacheka kumbali yake yakumanja, koma adzakhala ndi njala. Adzadya kumanzere kwake, koma sadzakhuta.+ Aliyense adzadya mnofu wa dzanja lake.+
14 Inuyo mudzadya koma simudzakhuta ndipo mudzamvabe njala.+ Mudzanyamula zinthu kuti mukazisunge pabwino koma simudzatha kuziteteza. Zinthu zilizonse zimene mudzazitenge, ine ndidzazipereka kwa adani anu kuti aziwononge.+
6 Mwafesa mbewu zambiri koma zokolola zanu n’zochepa.+ Mukudya koma simukukhuta.+ Mukumwa koma simukukhutira.* Mukuvala zovala koma simukumva kutentha. Amene akugwira ganyu akulandirira ndalama zake m’matumba obowoka.’”+