Levitiko 26:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndikadzathyola ndodo zanu zopachikapo mkate wozungulira woboola pakati,+ akazi 10 adzaphika mkate mu uvuni umodzi, ndipo adzakugawirani mochita kukuyezerani pamuyezo.+ Chotero mudzadya koma simudzakhuta.+ Deuteronomo 28:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Iwo adzadya chipatso cha ziweto zako ndi zipatso za nthaka yako kufikira utafafanizidwa,+ ndipo sadzakusiyirako mbewu, vinyo watsopano kapena mafuta, mwana wa ng’ombe yako kapena mwana wa nkhosa yako kufikira atakuwonongeratu.+
26 Ndikadzathyola ndodo zanu zopachikapo mkate wozungulira woboola pakati,+ akazi 10 adzaphika mkate mu uvuni umodzi, ndipo adzakugawirani mochita kukuyezerani pamuyezo.+ Chotero mudzadya koma simudzakhuta.+
51 Iwo adzadya chipatso cha ziweto zako ndi zipatso za nthaka yako kufikira utafafanizidwa,+ ndipo sadzakusiyirako mbewu, vinyo watsopano kapena mafuta, mwana wa ng’ombe yako kapena mwana wa nkhosa yako kufikira atakuwonongeratu.+