Salimo 105:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye anadzetsa njala yaikulu m’dzikomo,+Ndipo anathyola ndodo zonse zopachikapo mkate wozungulira woboola pakati.+ Ezekieli 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Ndikadzakutumizirani mivi yakupha yobweretsa njala+ imene idzakuwonongeni,+ ndidzachititsa kuti njala ikule pakati panu, ndipo ndidzathyola ndodo zimene mumakolowekapo mikate yozungulira yoboola pakati.+
16 Iye anadzetsa njala yaikulu m’dzikomo,+Ndipo anathyola ndodo zonse zopachikapo mkate wozungulira woboola pakati.+
16 “‘Ndikadzakutumizirani mivi yakupha yobweretsa njala+ imene idzakuwonongeni,+ ndidzachititsa kuti njala ikule pakati panu, ndipo ndidzathyola ndodo zimene mumakolowekapo mikate yozungulira yoboola pakati.+