Deuteronomo 32:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndidzawonjezera masoka awo,+Mivi yanga ndidzaithera pa iwo.+ Salimo 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye adzadzikonzera zida za imfa,+Ndipo adzapanga mivi yake kukhala yoyaka moto walawilawi.+