Salimo 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye adzadzikonzera zida za imfa,+Ndipo adzapanga mivi yake kukhala yoyaka moto walawilawi.+ Ezekieli 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Ndikadzakutumizirani mivi yakupha yobweretsa njala+ imene idzakuwonongeni,+ ndidzachititsa kuti njala ikule pakati panu, ndipo ndidzathyola ndodo zimene mumakolowekapo mikate yozungulira yoboola pakati.+
16 “‘Ndikadzakutumizirani mivi yakupha yobweretsa njala+ imene idzakuwonongeni,+ ndidzachititsa kuti njala ikule pakati panu, ndipo ndidzathyola ndodo zimene mumakolowekapo mikate yozungulira yoboola pakati.+