Deuteronomo 32:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndidzaledzeretsa mivi yanga ndi magazi,+Magazi a anthu ophedwa ndi ogwidwa.Ndipo lupanga langa lidzadya nyama,+Pamodzi ndi mitu ya atsogoleri a adani.’+ Salimo 45:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mivi yako yakuthwa idzalasa mitima ya adani a mfumu,+Mitundu ya anthu idzagwa pamapazi ako.+ Salimo 64:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Mulungu adzawalasa ndi muvi modzidzimutsa.+Iwo adzakhala ndi zilonda,+
42 Ndidzaledzeretsa mivi yanga ndi magazi,+Magazi a anthu ophedwa ndi ogwidwa.Ndipo lupanga langa lidzadya nyama,+Pamodzi ndi mitu ya atsogoleri a adani.’+