Yoswa 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno Yoswa analandira uthenga wakuti: “Mafumu asanu aja apezeka atabisala kuphanga la ku Makeda.”+ Yoswa 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako Yoswa anawakantha ndi kuwapha. Atatero anawapachika pamitengo isanu, pomwe anakhalapo mpaka madzulo.+ 1 Samueli 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma Samueli anati: “Monga mmene akazi anaferedwera ana awo chifukwa cha lupanga lako,+ momwemonso mayi ako+ aferedwa ana koposa akazi onse.”+ Pamenepo Samueli anadula Agagi nthulinthuli pamaso pa Yehova ku Giligala.+
17 Ndiyeno Yoswa analandira uthenga wakuti: “Mafumu asanu aja apezeka atabisala kuphanga la ku Makeda.”+
26 Kenako Yoswa anawakantha ndi kuwapha. Atatero anawapachika pamitengo isanu, pomwe anakhalapo mpaka madzulo.+
33 Koma Samueli anati: “Monga mmene akazi anaferedwera ana awo chifukwa cha lupanga lako,+ momwemonso mayi ako+ aferedwa ana koposa akazi onse.”+ Pamenepo Samueli anadula Agagi nthulinthuli pamaso pa Yehova ku Giligala.+