28 Munthu wamkazi anaima pawindo ndi kuyang’ana kunja, kumuyembekezera,
Amayi a Sisera anayang’ana kunja pawindo,+ kumuyembekezera, ndipo anati,
‘N’chifukwa chiyani galeta lake lankhondo lachedwa kubwera?+
N’chifukwa chiyani kuguguda kwa magaleta ake kwachedwa kumveka?’+