Oweruza 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo Yehova anayamba kusokoneza+ ndi kuwononga Sisera ndi magaleta ake onse ankhondo, pamodzi ndi anthu ake onse. Anawasokoneza ndi kuwawononga ndi lupanga pamaso pa Baraki. Zitatero Sisera anatsika m’galeta wake n’kuyamba kuthawa wapansi. 1 Samueli 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma Samueli anati: “Monga mmene akazi anaferedwera ana awo chifukwa cha lupanga lako,+ momwemonso mayi ako+ aferedwa ana koposa akazi onse.”+ Pamenepo Samueli anadula Agagi nthulinthuli pamaso pa Yehova ku Giligala.+
15 Pamenepo Yehova anayamba kusokoneza+ ndi kuwononga Sisera ndi magaleta ake onse ankhondo, pamodzi ndi anthu ake onse. Anawasokoneza ndi kuwawononga ndi lupanga pamaso pa Baraki. Zitatero Sisera anatsika m’galeta wake n’kuyamba kuthawa wapansi.
33 Koma Samueli anati: “Monga mmene akazi anaferedwera ana awo chifukwa cha lupanga lako,+ momwemonso mayi ako+ aferedwa ana koposa akazi onse.”+ Pamenepo Samueli anadula Agagi nthulinthuli pamaso pa Yehova ku Giligala.+