Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 9:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Aliyense wokhetsa magazi a munthu, nayenso magazi ake adzakhetsedwa ndi munthu,+ chifukwa Mulungu anapanga munthu m’chifaniziro chake.

  • Levitiko 24:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “‘Munthu aliyense amene wakantha ndi kupheratu mnzake, nayenso aziphedwa ndithu.+

  • Deuteronomo 19:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Diso lako lisamumvere chisoni.+ Pazikhala moyo kulipira moyo, diso kulipira diso, dzino kulipira dzino, dzanja kulipira dzanja, phazi kulipira phazi.+

  • Oweruza 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Zitatero, Adoni-bezeki anati: “Panali mafumu 70 odulidwa zala zamanthu za m’manja ndi zala zazikulu za kumapazi, amene anali kutola chakudya pansi pa tebulo langa. Mulungu wandibwezera zimene ndinachita.”+ Kenako anam’tengera ku Yerusalemu+ kumene anakafera.

  • Mateyu 7:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 pakuti chiweruzo chimene mukuweruza nacho ena inunso mudzaweruzidwa nacho.+ Ndipo muyezo umene mukuyezera ena, iwonso adzakuyezerani womwewo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena