Ekisodo 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ngati wina wamwalira, pamenepo uzipereka moyo kulipira moyo.+ Levitiko 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kuthyola fupa kulipira kuthyola fupa, diso kulipira diso, dzino kulipira dzino. Mmene wapundulira mnzake nayenso muzim’pundula chimodzimodzi.+ Mateyu 5:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “Inu munamva kuti anati, ‘Diso kulipira diso, ndi dzino kulipira dzino.’+
20 Kuthyola fupa kulipira kuthyola fupa, diso kulipira diso, dzino kulipira dzino. Mmene wapundulira mnzake nayenso muzim’pundula chimodzimodzi.+