Ekisodo 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma wina akavulaza mnzake koopsa, pazikhala diso kulipira diso, dzino kulipira dzino, dzanja kulipira dzanja, phazi kulipira phazi,+ Levitiko 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kuthyola fupa kulipira kuthyola fupa, diso kulipira diso, dzino kulipira dzino. Mmene wapundulira mnzake nayenso muzim’pundula chimodzimodzi.+ Deuteronomo 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Diso lako lisamumvere chisoni.+ Pazikhala moyo kulipira moyo, diso kulipira diso, dzino kulipira dzino, dzanja kulipira dzanja, phazi kulipira phazi.+
24 Koma wina akavulaza mnzake koopsa, pazikhala diso kulipira diso, dzino kulipira dzino, dzanja kulipira dzanja, phazi kulipira phazi,+
20 Kuthyola fupa kulipira kuthyola fupa, diso kulipira diso, dzino kulipira dzino. Mmene wapundulira mnzake nayenso muzim’pundula chimodzimodzi.+
21 Diso lako lisamumvere chisoni.+ Pazikhala moyo kulipira moyo, diso kulipira diso, dzino kulipira dzino, dzanja kulipira dzanja, phazi kulipira phazi.+