Ekisodo 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma wina akavulaza mnzake koopsa, pazikhala diso kulipira diso, dzino kulipira dzino, dzanja kulipira dzanja, phazi kulipira phazi,+ Deuteronomo 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Diso lako lisamumvere chisoni.+ Pazikhala moyo kulipira moyo, diso kulipira diso, dzino kulipira dzino, dzanja kulipira dzanja, phazi kulipira phazi.+ Mateyu 5:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “Inu munamva kuti anati, ‘Diso kulipira diso, ndi dzino kulipira dzino.’+
24 Koma wina akavulaza mnzake koopsa, pazikhala diso kulipira diso, dzino kulipira dzino, dzanja kulipira dzanja, phazi kulipira phazi,+
21 Diso lako lisamumvere chisoni.+ Pazikhala moyo kulipira moyo, diso kulipira diso, dzino kulipira dzino, dzanja kulipira dzanja, phazi kulipira phazi.+