Mateyu 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 chifukwa mmene mumaweruzira ena inunso adzakuweruzani choncho.+ Ndipo muyezo umene mukuyezera ena iwonso adzakuyezerani womwewo.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:2 Yesu—Ndi Njira, tsa. 90 Nsanja ya Olonda,5/15/2008, tsa. 94/1/1999, tsa. 5
2 chifukwa mmene mumaweruzira ena inunso adzakuweruzani choncho.+ Ndipo muyezo umene mukuyezera ena iwonso adzakuyezerani womwewo.+