Mateyu 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 pakuti chiweruzo chimene mukuweruza nacho ena inunso mudzaweruzidwa nacho.+ Ndipo muyezo umene mukuyezera ena, iwonso adzakuyezerani womwewo.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:2 Yesu—Ndi Njira, tsa. 90 Nsanja ya Olonda,5/15/2008, tsa. 94/1/1999, tsa. 5
2 pakuti chiweruzo chimene mukuweruza nacho ena inunso mudzaweruzidwa nacho.+ Ndipo muyezo umene mukuyezera ena, iwonso adzakuyezerani womwewo.+