Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 14:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ndiyeno pa nthawi ya ulonda wam’mawa,* Yehova ali mumtambo ndi moto woima njo ngati chipilala,+ anayang’ana gulu la Aiguputo, ndipo anachititsa Aiguputowo kusokonezeka.+

  • Yoswa 10:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pamenepo Yehova anasokoneza adaniwo pamaso pa Aisiraeli.+ Ndiyeno Aisiraeli anayamba kupha adaniwo kwadzaoneni ku Gibeoni,+ ndi kuwathamangitsa kulowera kuchitunda cha Beti-horoni. Ndipo anapitiriza kuwapha mpaka kukafika ku Azeka+ ndi ku Makeda.+

  • 2 Mafumu 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Yehova anali atachititsa anthu a mumsasa wa Asiriyawo kumva+ phokoso la magaleta ankhondo, phokoso la mahatchi, ndi phokoso la gulu lalikulu la asilikali amphamvu.+ Choncho anthuwo anauzana kuti: “Taonani! Mfumu ya Isiraeli yaitanitsa mafumu a Ahiti+ ndi mafumu a Iguputo+ kuti abwere kudzamenyana nafe!”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena