Deuteronomo 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Yehova adzachititsa adani ako amene adzakuukira kugonja pamaso pako.+ Pobwera kwa iwe adzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso pako, adzadutsa njira 7.+ 2 Samueli 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno ukakamva phokoso la kuguba pamwamba pa zitsamba za baka, pamenepo ukachitepo kanthu mwachangu,+ chifukwa pa nthawiyo Yehova adzakhala atatsogola kukapha gulu lankhondo la Afilisiti.”+ 2 Mafumu 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiika maganizo mwa iye,+ kuti akamva nkhani inayake,+ abwerere kudziko lake. Ndipo mosalephera ndidzachititsa kuti akaphedwe ndi lupanga m’dziko lake.”’”+
7 “Yehova adzachititsa adani ako amene adzakuukira kugonja pamaso pako.+ Pobwera kwa iwe adzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso pako, adzadutsa njira 7.+
24 Ndiyeno ukakamva phokoso la kuguba pamwamba pa zitsamba za baka, pamenepo ukachitepo kanthu mwachangu,+ chifukwa pa nthawiyo Yehova adzakhala atatsogola kukapha gulu lankhondo la Afilisiti.”+
7 Ndiika maganizo mwa iye,+ kuti akamva nkhani inayake,+ abwerere kudziko lake. Ndipo mosalephera ndidzachititsa kuti akaphedwe ndi lupanga m’dziko lake.”’”+