1 Mbiri 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno ukakamva phokoso la kuguba pamwamba pa zitsamba za baka,+ ukatuluke n’kumenyana nawo+ chifukwa Mulungu woona adzakhala atatsogola+ kukapha gulu lankhondo la Afilisiti.”
15 Ndiyeno ukakamva phokoso la kuguba pamwamba pa zitsamba za baka,+ ukatuluke n’kumenyana nawo+ chifukwa Mulungu woona adzakhala atatsogola+ kukapha gulu lankhondo la Afilisiti.”