Oweruza 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno usiku umenewo,+ Yehova anauza Gidiyoni kuti: “Nyamuka, pita kumsasa wa Amidiyani ndi kuuthira nkhondo, chifukwa ndaupereka m’manja mwako.+ 1 Samueli 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma akatiuza kuti, ‘Bwerani kuno mudzamenyane nafe!’ ife tipita chifukwa Yehova adzawaperekadi m’manja mwathu, ndipo chimenechi ndicho chizindikiro chathu.”+
9 Ndiyeno usiku umenewo,+ Yehova anauza Gidiyoni kuti: “Nyamuka, pita kumsasa wa Amidiyani ndi kuuthira nkhondo, chifukwa ndaupereka m’manja mwako.+
10 Koma akatiuza kuti, ‘Bwerani kuno mudzamenyane nafe!’ ife tipita chifukwa Yehova adzawaperekadi m’manja mwathu, ndipo chimenechi ndicho chizindikiro chathu.”+