-
Genesis 24:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Zichitike kuti, mtsikana amene ndimuuze kuti, ‘Chonde tula pansi mtsuko wako wa madzi kuti ndimweko,’ ndipo amenedi ati andiyankhe kuti, ‘Imwani, ndiponso nditungira madzi ngamila zanu kuti zimwe,’ ameneyo ndi amene mwasankhira mtumiki wanu+ Isaki. Mukachita zimenezo, ndidziwa kuti mwasonyeza mbuyanga chikondi chosatha.”+
-