Ekisodo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mulungu anapitiriza kuti: “Ngati sakakukhulupirira ndi kulabadira chizindikiro choyamba, akakhulupirira chizindikiro chachiwirichi.+ 1 Samueli 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, Sauli atangotembenuka kuti asiyane ndi Samueli, Mulungu anayamba kusintha mtima wake kukhala wina,+ moti zizindikiro+ zonsezi zinayamba kuchitikadi pa tsiku limenelo. Yeremiya 44:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Yehova wanena kuti: ‘Tsopano chizindikiro cha zimenezi kwa inu ndi ichi,+ ine ndikulangani m’dziko lino kuti mudziwe kuti mawu anga adzakwaniritsidwadi moti ndidzakugwetserani tsoka.+
8 Mulungu anapitiriza kuti: “Ngati sakakukhulupirira ndi kulabadira chizindikiro choyamba, akakhulupirira chizindikiro chachiwirichi.+
9 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, Sauli atangotembenuka kuti asiyane ndi Samueli, Mulungu anayamba kusintha mtima wake kukhala wina,+ moti zizindikiro+ zonsezi zinayamba kuchitikadi pa tsiku limenelo.
29 “Yehova wanena kuti: ‘Tsopano chizindikiro cha zimenezi kwa inu ndi ichi,+ ine ndikulangani m’dziko lino kuti mudziwe kuti mawu anga adzakwaniritsidwadi moti ndidzakugwetserani tsoka.+