Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 2:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Ndipo chizindikiro chako chimene chidzachitikira ana ako awiri Hofeni ndi Pinihasi+ ndi ichi: Onse awiri adzafa tsiku limodzi.+

  • 1 Samueli 10:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno zizindikiro+ zimenezi zikachitika pa iwe, uchite chilichonse chimene ungathe,+ chifukwa Mulungu woona ali ndi iwe.+

  • 2 Mafumu 20:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Yesaya anayankha kuti: “Chizindikiro+ chochokera kwa Yehova, chakuti Yehova adzakwaniritsadi mawu amene walankhula, ndi ichi: Kodi mthunzi uyende masitepe 10 kupita kutsogolo, kapena uyende masitepe 10 kubwerera m’mbuyo pamasitepe olowera m’nyumba?”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena