-
Oweruza 9:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Ndiyeno mawa mudzuke mwamsanga dzuwa likangotuluka, ndi kuthamangira mumzindawo. Ndipo iye ndi anthu amene ali nawo akatuluka kudzamenyana nanu, mum’chitire zimene mungathe kuti mum’gonjetse.”
-