1 Samueli 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno zizindikiro+ zimenezi zikachitika pa iwe, uchite chilichonse chimene ungathe,+ chifukwa Mulungu woona ali ndi iwe.+ Yesaya 38:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chizindikiro chochokera kwa Yehova, chakuti Yehova adzakwaniritsadi mawu amene walankhula, ndi ichi:+
7 Ndiyeno zizindikiro+ zimenezi zikachitika pa iwe, uchite chilichonse chimene ungathe,+ chifukwa Mulungu woona ali ndi iwe.+
7 Chizindikiro chochokera kwa Yehova, chakuti Yehova adzakwaniritsadi mawu amene walankhula, ndi ichi:+