Oweruza 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo iye anati: “Tsopano ngati mwandikomera mtima,+ mundisonyeze chizindikiro kuti nditsimikize kuti ndinudi amene mukulankhula nane.+ Oweruza 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno iwo anamuuza kuti: “Tifunsire+ kwa Mulungu+ kuti tidziwe ngati kumene tikupita tidzayendako bwino.”
17 Pamenepo iye anati: “Tsopano ngati mwandikomera mtima,+ mundisonyeze chizindikiro kuti nditsimikize kuti ndinudi amene mukulankhula nane.+
5 Ndiyeno iwo anamuuza kuti: “Tifunsire+ kwa Mulungu+ kuti tidziwe ngati kumene tikupita tidzayendako bwino.”